ChewaGPT
ChewaGPT ndi ntchito yobweretsa ChatGPT m'Chichewa. Chonde, tsimikizani zakulondola kwa mayankho omwe mungapeze pogwiritsa ChewaGPT kamba koti pena mayankhowa amakhala osalondola. iHubOnline siidzayankha kalikonse pazotsatira zomwe zingakugwereni kamba kogwiritsa ChewaGPT.